Mawu a M'munsi
a M’Baibulo la The Jerusalem Bible, mawu a m’munsi pa Genesis 2:17, amati “kudziŵa zabwino ndi zoipa” ndiko “kutha kusankha . . . zabwino ndi zoipa ndi kuchita malinga ndi zomwe wasankhazo, kunena kuti ndi wodziimira payekha zimene zimachititsa munthu kusavomereza kuti anachita kulengedwa.” Mawuwo akupitiriza kuti: “Tchimo loyambali linaukira ulamuliro wa Mulungu.”