Mawu a M'munsi
b Buku lotchedwa Keil-Delitzsch Commentary on the Old Testament, Voliyumu 1, patsamba 148, limati: “Tingati patatha masiku 73 chingalawa chitatera, nsonga za mapiri zinaoneka, zimene zinali nsonga za mapiri a ku Armenia amene anazungulira chingalawacho.”