Mawu a M'munsi
a Pamene Yesu Kristu anakwera kumwamba n’kupereka kwa Yehova Mulungu mtengo wa moyo wake waumunthu woperekedwa nsembe, pangano la Chilamulo cha Mose linathetsedwa, ndipo maziko a “pangano latsopano” lonenedweratulo anakhazikitsidwa.—Yeremiya 31:31-34.