Mawu a M'munsi
a Nthenda ya multiple sclerosis imasokoneza ubongo ndi fupa la msana. Nthaŵi zambiri, matendawa pang’onopang’ono amayambitsa chizungulire, amawononga miyendo ndi mikono, ndiponso nthaŵi zina amamuchititsa munthu kuvutikira kuona, kulankhula, kapena kumvetsa zinthu.