Mawu a M'munsi
c Mfundo zisanu ndi zitatu zimene anazitchula m’nkhaniyo ndi izi: (1) Musakhale Wosakhazikika Mtima; (2) Khalani ndi Maganizo Abwino; (3) Tsegulani Maganizo Anu ku Mitundu Yatsopano ya Ntchito; (4) Dalirani pa Ndalama Zimene Mumapeza—Osati za Wina; (5) Chenjerani ndi Ngongole; (6) Lisungeni Banja Kukhala Logwirizana; (7) Sungani Ulemu Wanu Waumwini; (8) Pangani Bajeti.