Mawu a M'munsi
a Mzera umene Yesu anadzabadwiramo umene unalembedwa ndi Mateyu umatchula mayina a akazi anayi omwe ndi Tamara, Rahabi, Rute, ndi Mariya. Akazi onseŵa amalemekezedwa kwambiri m’Mawu a Mulungu.—Mateyu 1:3, 5, 16.