Mawu a M'munsi
a Ku tsango lililonse la zipatso za mtengowu kumatha kukhala zipatso 1,000 ndipo tsangolo limatha kulemera makilogalamu eyiti kapena kupitirira pamenepo. Wolemba mabuku wina anati “munthu akakhala ndi mitengo yobereka [ya migwalangwa] amatha kupeza zipatso zolemera matani aŵiri kapena atatu pa mtengo uliwonse panthaŵi yomwe mtengowo uli ndi moyo.”