Mawu a M'munsi
d Nthaŵi zambiri, mankhwala enieni m’majekeseni ena kapena mankhwala ofunika kwambiri m’majekeseniwo sawatenga m’magazi. Koma nthaŵi zina mbali yochepa chabe ya mankhwalawo imatha kukhala kachigawo kakang’ono ka magazi, monga albumin.—Onani “Mafunso Ochokera kwa Oŵerenga” mu Nsanja ya Olonda ya October 1, 1994.