Mawu a M'munsi
a M’nthaŵi za m’Baibulo, adani amene anagwidwa, monga Samsoni ndi Aisrayeli ena, anali kuwagwiritsa ntchito yopera mbewu. (Oweruza 16:21; Maliro 5:13) Azimayi ena ankapera mbewu za pabanja pawo ngakhale kuti sanali akapolo.—Yobu 31:10.