Mawu a M'munsi
a M’malo mwa mawu akuti “odala,” mabaibulo ena, monga The Jerusalem Bible ndi Today’s English Version, amati “achimwemwe.” Motero, m’nkhani ino ndi m’nkhani yotsatirayi tigwiritsa ntchito mawu akuti “achimwemwe,” pofotokozera malemba amene akutchula mawu akuti “odala.”