Mawu a M'munsi
b N’zomvetsa chisoni kuti Mbale Michal Žobrák anatisiya. Anamwalira nkhani ino ikukonzedwa kuti ifalitsidwe ndipo anali wokhulupirika komanso anali ndi chiyembekezo cholimba chakuti adzaukitsidwa.