Mawu a M'munsi
a M’chigiriki choyambirira, mawu omwe anawamasulira kuti “zowawa” amatanthauza “ululu wobereka.” (Mateyu 24:8) Izi zikusonyeza kuti mofanana ndi ululu wobereka, mavuto adzikoli ayamba kuchitika pafupifupi, azikhala owawa kwambiri, ndiponso azitenga nthawi yaitali kusiyana ndi m’mbuyomu, ndipo mapeto ake chidzafika chisautso chachikulu.