Mawu a M'munsi
a Zinali kwa munthu amene akulumbirayo kudzisankhira kutalika kwa nthawi yomwe akufuna kukhala Mnaziri. Koma, malinga ndi nkhani zakale za Ayuda, nthawi yomwe munthu angakhale Mnaziri inkayambira pa masiku 30. Ankaganiza kuti kupanga lumbiro la masiku osakwana 30 kukanachitititsa kuti lumbiroli lingokhala ngati lumbiro wamba.