Mawu a M'munsi
a M’nkhani ino, mawu akuti “zozizwitsa” akutanthauza zimene buku lina lotanthauzira mawu a m’Baibulo limanena kuti: “Zochitika m’dziko lapansi zomwe sizingatheke ndi mphamvu iliyonse yaumunthu kapena yachilengedwe ndipo motero anthu amakhulupirira kuti zimachitika ndi mphamvu zauzimu.”