Mawu a M'munsi
a Mawu achigiriki akuti chikumbumtima amene agwiritsidwa ntchito palembali amatanthauza “mphamvu ya m’mtima yozindikira khalidwe labwino” (The Analytical Greek Lexicon Revised, yolembedwa ndi Harold K. Moulton); “kusiyanitsa khalidwe labwino ndi loipa.”—Greek-English Lexicon, yolembedwa ndi J. H. Thayer.