Mawu a M'munsi
a Mabaibulo ena amachotsa mawu oti “mkono” m’vesili n’kuikapo muyeso wa nthawi, monga “kamphindi” (The Emphatic Diaglott) kapena “mphindi imodzi” (A Translation in the Language of the People, la Charles B. Williams). Koma mawu amene anagwiritsidwa ntchito m’malemba oyambirira amatanthauza muyeso wa masentimita pafupifupi 45.