Mawu a M'munsi
a Malinga ndi buku lakuti Encyclopaedia Judaica, alimi a ku Israyeli ankakonda mipesa imene inkabereka mphesa zofiira moderako, zomwe mwina n’zimene zatchulidwa pa Yesaya 5:2. Mphesa zimenezi zinkatulutsa vinyo wofiira wotsekemera.