Mawu a M'munsi b Ataliyana osamuka kwawo pafupifupi 1,000,000 anakhazikika ku São Paulo pakati pa 1870 ndi 1920.