Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO

Mawu a M'munsi

a Kale, Mfumu Davide ya Israyeli inalanda Ajebusi phiri la Ziyoni la padziko lapansi pano, n’kulisandutsa likulu la ufumu wake. (2 Samueli 5:6, 7, 9) Inasamutsanso Likasa lopatulika n’kupita nalo komweko. (2 Samueli 6:17) Popeza Likasa linkaimira kukhalapo kwa Yehova, Ziyoni ankatchedwa malo omwe Mulungu ankakhala, zomwe zinachititsa kuti malowa akhale oyenera kuimira kumwamba.​—Eksodo 25:22; Levitiko 16:2; Salmo 9:11; Chivumbulutso 11:19.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena