Mawu a M'munsi
b Ngati mwamuna ndi mkazi akonza zoti munthu wina adzajambule zithunzi kapena vidiyo ya ukwatiwo pa Nyumba ya Ufumuyo, ayenera kuoneratu nthawi ikadalipo kuti sipadzakhala chilichonse chimene chingadzanyozetse ukwatiwo.