Mawu a M'munsi
a Kuti mumvetse bwino tanthauzo la fanizo limeneli, werengani Luka 17:22-33. Onani mmene zimene zalembedwa pa Luka 17:22, 24, 30, zonena za “Mwana wa munthu” zikutithandizira kuyankha funso lomwe lili pa Luka 18:8.