Mawu a M'munsi
a Pofika m’chaka cha 1835, Baibulo linali litamasuliridwa m’chinenero cha ku Madagascar chotchedwa Chimalagase, ndipo pofika m’chaka cha 1840, m’chinenero cha ku Ethiopia chotchedwa Chiamuhariki. Koma Baibulo lisanamasuliridwe, zinthu zina zinali zitalembedwapo kalekale m’zinenerozi.