Mawu a M'munsi
a Baibulo limatcha likulu la kulambira koonali kuti ndi “kachisi” wa Yehova. Komabe, panthawiyi likasa la chipangano linkakhala mu chihema. Kachisi weniweni woyamba anamangidwa mu ulamuliro wa Mfumu Solomo.—1 Samueli 1:9; 2 Samueli 7:2, 6; 1 Mafumu 7:51; 8:3, 4.