Mawu a M'munsi
c Katswiri wina wa maphunziro a Baibulo, yemwe ndi Myuda, dzina lake Alfred Edersheim anati: “Aisiraeli anali asanaonepo zoopsa zoterezi n’kale lonse, ndipo ngakhale patsogolo pake sanadzaonepo zoopsa zochita kufika pamenepa.”