Mawu a M'munsi
a Aroma ndi Agiriki m’nthawi ya atumwi, sankalola mkazi kukwatiwa ndi amuna angapo nthawi imodzi. Choncho, panalibe chifukwa choti Paulo alembere Timoteyo za nkhani imeneyi, kapena kudzudzula munthu amene anali kuchita zimenezi.