Mawu a M'munsi
a Kuti mudziwe zambiri zokhudza mmene mungathandizire makolo amene akulira maliro a mwana wawo, onani mutu wakuti “Kodi Ena Angathandize Motani?” pa tsamba 20 mpaka 24 m’kabuku kakuti Pamene Munthu Amene Mumakonda Amwalira, kofalitsidwa ndi Mboni za Yehova.