Mawu a M'munsi
a Dzina lenileni la mngelo amene anakhala Satana silikudziwika. Mayina akuti “Satana” ndi “Mdyerekezi” amatanthauza “Wotsutsa” ndi “Woneneza.” Zimene Satana anachita zimafananako ndi zomwe mfumu yakale ya Turo inachita. (Ezekieli 28:12-19) Poyamba onse anali angwiro m’zochita zawo koma anayamba kudzikuza.