Mawu a M'munsi
a Panthawiyi, dera la kum’mawa la chilumbachi linagawidwa pawiri; chakum’mwera kunali Papua ndipo chakumpoto kunali New Guinea. Masiku ano, dera la kumadzulo kwa chilumbachi limatchedwa Papua, ndipo ndi mbali ya dziko la Indonesia. Dera la kum’mawa limatchedwa Papua New Guinea.