Mawu a M'munsi
a Anthu samvana chimodzi pankhani ya kugwirizana kwa ndandanda ya pa Kalendala ya Gezeri ndi miyezi imene Baibulo limatchula. Komanso, m’madera osiyanasiyana a m’Dziko Lolonjezedwa, ntchito zina zaulimi zinkachitika pa nthawi yosiyanako pang’ono.