Mawu a M'munsi
a Mlongo Stigers anamaliza utumiki wake wa padziko lapansi pa April 20, 2007, kutangotsala miyezi itatu kuti akwanitse zaka 100. Tikulimbikitsidwa kwambiri ndi zaka zambiri zomwe wakhala akutumikira mokhulupirika ndipo tikusangalala kuti walandira mphoto yake kumwamba.