Mawu a M'munsi
a M’nkhani ino, “Chipangano Chakale” chikutchedwa Malemba Achiheberi. (Onani bokosi loti “Chipangano Chakale kapena Malemba Achiheberi?” patsamba 6.) Mboni za Yehova zimatchulanso “Chipangano Chatsopano” kuti Malemba Achigiriki Achikristu.