Mawu a M'munsi
a Magazini a Nsanja ya Olonda tsopano azituluka awiri osiyana. Magazini ya pa 1 mwezi uliwonse ndi yogawira anthu onse ndipo ya pa 15 ndi imene Mboni za Yehova ziziphunzira pa misonkhano yawo ya mpingo imene aliyense ali wolandiridwa kufikapo.