Mawu a M'munsi
a Kuti muwerenge mfundo zina zotsutsa bodza lakuti maulosi a m’Baibulo analembedwa zinthuzo zitachitika kale, onani masamba 106 mpaka 111 a buku lachingelezi lakuti Is There a Creator Who Cares About You? Lofalitsidwa ndi Mboni za Yehova.