Mawu a M'munsi a Nkhani ngati yomweyi imapezeka mu Uthenga Wabwino wa Luka, ndipo imasonyeza kuti Yehova anagwiritsa ntchito m’lowam’malo wakuti “iwe” motere: “Iwe ndiwe Mwana wanga wokondedwa; ndimakondwera nawe.”—Luka 3:22.