Mawu a M'munsi
a Mtumwi Paulo anagwiritsa ntchito liwu lovuta kulimasulira ndi mawu amodzi. Buku lina limati: “Liwulo limanena za mtima umene umalolera kudzimana ufulu wako ndiponso woganizira ena komanso wachifundo.” Choncho mfundo ya liwulo imaphatikizapo kukhala wololera, osati kuumiriza munthu kuti atsatire malamulo mosaphonyetsako kapena kuumirira kuti ndi ufulu wanga kuchita zakutizakuti.