Mawu a M'munsi
a Mwambowu umatchedwanso Mgonero wa Ambuye, kunyema buledi, msonkhano wa Ukalisitiya, Nsembe, ndiponso Misa. Mawu akuti “Ukalisitiya” anachokera ku mawu a Chigiriki akuti eu·kha·ri·sti΄a, omwe amatanthauza kuyamika, kuthokoza, kapena kuyamikira.