Mawu a M'munsi
a Mlembi wa mpingo akangodziwa kuti m’bale kapena mlongo wina mumpingo wawo wasamukira ku malo osungirako okalamba m’dera lina, angachite bwino kudziwitsa akulu a m’dera limenelo mwamsanga.