Mawu a M'munsi
b “Zombo za ku Tarisi” za Solomo zinkagwira ntchito pamodzi ndi za Hiramu, ndipo mwina zinkachita malonda kunja kwa dera lotchedwa Ezioni Geberi ndiponso zinkafika ku Nyanja Yofiira ndi madera ena akutali.—1 Mafumu 10:22.