Mawu a M'munsi
a Nyumba za Ufumu zina zili ndi zithunzi za anthu a m’Baibulo. Komabe, zithunzi zimenezi n’zongokongoletsera nyumbayo, ndipo sizimalambiridwa. Mboni za Yehova sizigwiritsa ntchito zithunzi zimenezi popemphera komanso samazigwadira.