Mawu a M'munsi
a Zikuoneka kuti dzina lakuti Davide limatanthauza kuti “Wokondedwa.” Ndipo pa ubatizo wa Yesu komanso atasandulika, Yehova analankhula kuchokera kumwamba ndipo anamutcha kuti, “mwana wanga wokondedwa.”—Mat. 3:17; 17:5.