Mawu a M'munsi
a Mabaibulo ena amamasulira lembali mosonyeza kuti munthu angalandire chilango cha imfa chifukwa cha imfa ya mayi yokha. Komabe, m’Chiheberi choyambirira lembali limasonyeza kuti lamuloli linkanena za imfa ya mayi kapena ya mwana wake wosabadwa.