Mawu a M'munsi
a Sikuti Mose anaonadi Yehova, chifukwa palibe munthu yemwe angaone Mulungu n’kukhalabe ndi moyo. (Eksodo 33:20) Koma Yehova anaonetsa Mose masomphenya a ulemerero Wake, ndipo analankhula naye kudzera mwa mngelo.