Mawu a M'munsi
a N’kutheka kuti Asa anachotsa misanje ya milungu yonyenga koma osati imene inali pamalo amene anthu ankalambirirapo Yehova. Apo ayi, ndiye kuti misanjeyo inamangidwanso pambuyo pa ulamuliro wa Asa, ndipo mwana wake Yehosafati atayamba kulamulira anachotsa misanjeyo.—1 Maf. 15:14; 2 Mbiri 15:17.