Mawu a M'munsi
d Zina mwa ziphunzitso zimenezi ndi zokhudza ulamuliro wa Mulungu, kukhulupirika kwa anthu, nkhani yokhudza chabwino ndi choipa, ufulu wosankha zochita, mmene akufa alili, ukwati, Mesiya wolonjezedwa, dziko laparadaiso, Ufumu wa Mulungu ndi zina zambiri.