Mawu a M'munsi
e Kuti mumve zambiri, onani buku lofalitsidwa ndi Mboni za Yehova lakuti, Kodi Baibulo Limaphunzitsa Chiyani Kwenikweni? mutu 3, wakuti, “Kodi Mulungu Ali Nalo Cholinga Chotani Dziko Lapansili?,” ndi mutu 5, wakuti, “Dipo la Yesu Ndilo Mphatso ya Mulungu ya Mtengo Wapatali Koposa Zonse.”