Mawu a M'munsi
a M’Chichewa, dzina lakuti Yakobe ndi lofanana ndi lakuti Yakobo. Mawu akuti “Abulahamu, Isake ndi Yakobo” amapezeka nthawi zambiri m’Baibulo. Ndipo lemba la Mateyo 1:16, limatchula za Yakobo, yemwe “anabala Yosefe, mwamuna wake wa Mariya.”