Mawu a M'munsi
a Tischendorf anatchuka kwambiri chifukwa chotulukira Baibulo la Malemba a Chiheberi akale kwambiri omasuliridwa m’Chigiriki. Iye analipeza ku tchalitchi cha St. Catherine chomwe chili mphepete mwa Phiri la Sinai. Ndipo Baibulo limeneli limatchedwa Codex Sinaiticus.