Mawu a M'munsi b M’buku lonse la Deuteronomo, Mose anatsindika mfundo yakuti chinthu chofunika kwambiri kwa anthu onse okhulupirika ndi kuopa Mulungu.—Deuteronomo 4:10; 6:13, 24; 8:6; 13:4; 31:12, 13.