Mawu a M'munsi
a Baibulo la Vatican Codex limatchedwanso Vatican Manuscript 1209 kapena Codex Vaticanus, ndipo akatswiri a Baibulo ambiri amangolitchula kuti “B.” Baibuloli ndi lakale kwambiri ndipo mabuku a masiku ano amapangidwa mofananako ndi Baibulo limeneli. Onani nkhani yakuti: “Mmene Mipukutu Inafikira Pokhala Baibulo Lathunthu,” mu Nsanja ya Olonda ya June 1, 2007.