Mawu a M'munsi
a Mbali zina za Baibulo zinalembedwa m’Chialamu, chinenero chofanana kwambiri ndi Chiheberi chimene anagwiritsa ntchito polemba Baibulo. Mbali zake ndi monga Ezara 4:8 mpaka 6:18 ndi 7:12-26, Yeremiya 10:11, ndi Danieli 2:4b mpaka 7:28.